Eksodo 36:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anaika magango ansalu yamadzi m'mphepete mwake mwa nsalu imodzi ku mkawo wa chilumikizano; nachita momwemo m'mphepete mwake mwa nsalu ya kuthungo, ya chilumikizano chachiwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anaika magango ansalu yamadzi m'mphepete mwake mwa nsalu imodzi ku mkawo wa chilumikizano; nachita momwemo m'mphepete mwake mwa nsalu ya kuthungo, ya chilumikizano chachiwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pambuyo pake adasoka magonga a tinsalu tobiriŵira m'mphepete mwa chimodzi kubwalo kwake, ndipo adachitanso chimodzimodzi ndi chinacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka anapanga zokolowekamo za nsalu yobiriwira mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsiriza ya mbali ina. Ndipo anachita chimodzimodzi ndi nsalu yotsiriza ya mbali inayo. Onani mutuwo |