Eksodo 35:16 - Buku Lopatulika16 guwa la nsembe yopsereza, ndi sefa wamkuwa, mphiko zake, ndi zipangizo zake zonse, mkhate ndi tsinde lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 guwa la nsembe yopsereza, ndi sefa wamkuwa, mphiko zake, ndi zipangizo zake zonse, mkhate ndi tsinde lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Apangenso guwa la zopereka zopsereza pamodzi ndi chitsolo cha sefa yamkuŵa, mphiko zake ndi zipangizo zake zomwe, beseni losambira ndi phaka lake lomwe; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 guwa lansembe yopsereza pamodzi ndi sefa yamkuwa, mitengo yake yonyamulira ndi zipangizo zake zonse, beseni losambira lamkuwa ndi miyendo yake; Onani mutuwo |