Eksodo 35:17 - Buku Lopatulika17 nsalu zotchingira za kubwalo, nsichi zake, ndi makamwa ake, ndi nsalu yotsekera ku chipata cha pabwalo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 nsalu zochingira za kubwalo, nsichi zake, ndi makamwa ake, ndi nsalu yotsekera ku chipata cha pabwalo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 nsalu zochinga bwalo, nsanamira pamodzi ndi masinde ake omwe, nsalu za pa chipata choloŵera ku bwalo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 nsalu yotchingira bwalo pamodzi ndi mizati yake ndi matsinde ake, ndiponso nsalu yotchingira pa khomo lolowera ku bwalo; Onani mutuwo |