Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 35:12 - Buku Lopatulika

12 likasa, ndi mphiko zake, chotetezerapo, ndi nsalu yotchinga yotseka;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 likasa, ndi mphiko zake, chotetezerapo, ndi nsalu yotchinga yotseka;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Apangenso bokosi lachipangano ndi mphiko zake, chivundikiro chake cha bokosilo ndi nsalu zotchinga bokosilo;

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Bokosi la Chipangano pamodzi ndi mitengo yake yonyamulira ndiponso chovundikira chake cha bokosilo ndi nsalu zophimba bokosilo;

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 35:12
5 Mawu Ofanana  

Ndipo uziomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale chophimba pamwamba pa chihema; uziomba nsalu khumi ndi imodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa