Eksodo 35:13 - Buku Lopatulika13 gome, ndi mphiko zake, ndi zipangizo zake zonse, ndi mkate woonekera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 gome, ndi mphiko zake, ndi zipangizo zake zonse, ndi mkate woonekera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 tebulo, pamodzi ndi mphiko zake ndi zipangizo zake, ndiponso buledi woperekedwa kosalekeza kwa Mulungu; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 tebulo pamodzi ndi mitengo yake yonyamulira pamodzi ndi zipangizo zake zonse ndiponso buledi wokhala pamaso pa Yehova; Onani mutuwo |