Eksodo 35:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israele, nanena nao, Siwa mau amene Yehova analamula, kuti muwachite. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israele, nanena nao, Siwa mau amene Yehova anauza, kuti muwachite. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mose adaitana Aisraele onse naŵauza kuti, “Chauta akukulamulani kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mose anasonkhanitsa gulu lonse la Aisraeli ndipo anawawuza kuti, “Zinthu zimene Yehova wakulamulirani kuti muzichite ndi izi: Onani mutuwo |