Eksodo 34:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Mose atatha kulankhula nao, anaika chophimba pankhope pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Mose atatha kulankhula nao, anaika chophimba pankhope pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Mose atamaliza kulankhula nawo, adadziphimba kumaso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Mose atamaliza kuyankhula nawo anaphimba nkhope yake. Onani mutuwo |