Eksodo 34:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo atatero, ana onse a Israele anayandikiza; ndipo iye anawauza zonse Yehova adalankhula naye m'phiri la Sinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo atatero, ana onse a Israele anayandikiza; ndipo iye anawauza zonse Yehova adalankhula naye m'phiri la Sinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pambuyo pake Aisraele onse adasendera pafupi, ndipo Mose adaŵapatsa malamulo onse amene Chauta adaamuuza ku phiri la Sinai lija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Kenaka Aisraeli onse anamuyandikira, ndipo anawapatsa malamulo onse omwe Yehova anamupatsa pa Phiri la Sinai. Onani mutuwo |