Eksodo 33:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anthu onse anaona mtambo njo ulikuima pakhomo pa chihema; ndi anthu onse anaimirira, nalambira, yense pakhomo pa hema wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anthu onse anaona mtambo njo ulikuima pakhomo pa chihema; ndi anthu onse anaimirira, nalambira, yense pakhomo pa hema wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndipo anthu ankati akaona mtambowo pa khomo la chihemacho, ankaimirira ndi kupembedza, aliyense pa khomo la hema lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nthawi zonse anthu akaona chipilala cha mtambo chitayima pa khomo la tentiyo amayimirira ndi kupembedza, aliyense ali pa khomo la tenti yake. Onani mutuwo |