Eksodo 32:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo pamene Yoswa anamva phokoso la kufuula kwa anthu, anati kwa Mose, Kuli phokoso la nkhondo kuchigono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo pamene Yoswa anamva phokoso la kufuula kwa anthu, anati kwa Mose, Kuli phokoso la nkhondo kuchigono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono Yoswa adamva anthu akufuula, nauza Mose kuti, “Ndikumva phokoso lankhondo kumahemako.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pamene Yoswa anamva phokoso la anthu anati kwa Mose, “Ku msasa kuli phokoso la nkhondo.” Onani mutuwo |