Eksodo 30:9 - Buku Lopatulika9 Musafukizapo chofukiza chachilendo, kapena nsembe yopsereza, kapena nsembe yaufa; musathirepo nsembe yothira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Musafukizapo chofukiza chachilendo, kapena nsembe yopsereza, kapena nsembe yaufa; musathirepo nsembe yothira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Paguwapo usafukizepo lubani wosaloledwa, kapena zopereka za nyama yopsereza kapena za zakudya. Usadzaperekenso pamenepo chopereka cha chakumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa guwapo usafukize lubani wachilendo kapena kuperekapo nsembe yopsereza kapena nsembe yaufa. Usathire pa guwapo ngakhale nsembe yachakumwa. Onani mutuwo |