Eksodo 30:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa guwapo usafukize lubani wachilendo kapena kuperekapo nsembe yopsereza kapena nsembe yaufa. Usathire pa guwapo ngakhale nsembe yachakumwa. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Musafukizapo chofukiza chachilendo, kapena nsembe yopsereza, kapena nsembe yaufa; musathirepo nsembe yothira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Musafukizapo chofukiza chachilendo, kapena nsembe yopsereza, kapena nsembe yaufa; musathirepo nsembe yothira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Paguwapo usafukizepo lubani wosaloledwa, kapena zopereka za nyama yopsereza kapena za zakudya. Usadzaperekenso pamenepo chopereka cha chakumwa. Onani mutuwo |