Eksodo 30:15 - Buku Lopatulika15 Wachuma asachulukitsepo, ndi osauka asachepse pa limodzi mwa magawo awiri a sekeli, pakupereka chopereka kwa Yehova, kuchita choteteza cha miyoyo yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Wachuma asachulukitsepo, ndi osauka asachepse pa limodzi mwa magawo awiri a sekeli, pakupereka chopereka kwa Yehova, kuchita choteteza cha miyoyo yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Wolemera asadzapereke kopitirira, ndipo wosauka asadzapereke mochepera pa theka la sekeli, pamene muzikapereka kwa Chauta zopereka zimenezi, kuti muwombole moyo wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Anthu olemera asapereke koposa theka la sekeli ndipo osauka asapereke kuchepera theka la sekeli pamene mukupereka nsembe kwa Yehova yowombolera miyoyo yanu. Onani mutuwo |