Eksodo 29:23 - Buku Lopatulika23 ndi mkate wamphumphu umodzi, ndi kamtanda ka mkate wosakaniza ndi mafuta, ndi kamtanda kamodzi kaphanthi, zili mu dengu la mkate wopanda chotupitsa wokhala pamaso pa Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndi mkate wamphumphu umodzi, ndi kamtanda ka mkate wosanganiza ndi mafuta, ndi kamtanda kamodzi kaphanthi, zili mu dengu la mkate wopanda chotupitsa wokhala pamaso pa Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 M'lichero limene lili m'Nyumba ya Chauta utengeko buledi mmodzi wosafufumitsa, keke imodzi yosakaniza ndi mafuta, ndiponso buledi mmodzi wopsapsalala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Utengenso mʼdengu la buledi wopanda yisiti limene lili pamaso pa Yehova, buledi mmodzi, buledi wokhala ndi mafuta a olivi, ndi buledi wopyapyala mmodzi. Onani mutuwo |