Eksodo 28:6 - Buku Lopatulika6 Naombe efodi ndi golide, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya mmisiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Naombe efodi ndi golide, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya mmisiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Efodi aisoke ndi nsalu yagolide, ndi nsalu yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndiponso ya bafuta wosalala, wopikidwa bwino ndi wopetedwa mwaluso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Apange efodi pogwiritsa ntchito golide, nsalu yamtundu wa mtambo, yapepo ndi yofiira yolukidwa mwaluso. Onani mutuwo |