Eksodo 28:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo atenge golide, ndi lamadzi ndi lofiirira ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo atenge golide, ndi lamadzi ndi lofiirira ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Zovala zimenezi anthu alusowo azisoke ndi nsalu yagolide, ndi nsalu yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndiponso ya bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo agwiritse ntchito golide, nsalu yamtundu wa mtambo, yapepo, yofiira ndi yosalala yofewa. Onani mutuwo |