Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 28:7 - Buku Lopatulika

7 Akhale nazo zapamapewa ziwiri zomangika ku nsonga zake ziwiri, kuti amangike nazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Akhale nazo zapamapewa ziwiri zomangika ku nsonga zake ziwiri, kuti amangike nazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Idzakhale ndi tizikwewo tam'mapewa tiŵiri tosokerera ku nsonga zake ziŵiri, tomangira efodiyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Efodiyo ikhale ndi timalamba tiwiri ta pa mapewa tosokerera ku msonga zake ziwiri kuti azitha kumanga.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 28:7
5 Mawu Ofanana  

Koma nsonga zake ziwiri za maunyolo opotawo uzimange ku zoikamo ziwiri, ndi kuziika pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'tsogolo mwake.


Naombe efodi ndi golide, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya mmisiri.


Ndipo mpango wa efodi, wokhala pamenepo, kuti ammange nao, ukhale wa chiombedwe chomwecho, ndi woombera kumodzi, wagolide, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.


Ndi nsonga zake ziwiri zina za maunyolo awiri opotawo anazimanga pa zoikamo ziwiri, nazimanga pa zapamapewa za efodi, m'tsogolo mwake.


Anapangira efodi zapamapewa zolumikizana; pansonga ziwirizo anamlumikiza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa