Eksodo 28:23 - Buku Lopatulika23 Nupangire pa chapachifuwa mphete ziwiri zagolide, ndi kuzika mphete ziwirizo pansonga zake ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Nupangire pa chapachifuwa mphete ziwiri zagolide, ndi kuzika mphete ziwirizo pa nsonga zake ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Upangenso mphete ziŵiri, ndipo uzilumikize pa ngodya zam'mwamba za chovala chapachifuwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Upangenso mphete ziwiri zagolide ndipo uzimangirire pa ngodya ziwiri za pa chovala chapachifuwa. Onani mutuwo |