Eksodo 28:22 - Buku Lopatulika22 Upangenso maunyolo pa chapachifuwa ngati zingwe, ntchito yopota, ya golide woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Upangenso maunyolo pa chapachifuwa ngati zingwe, ntchito yopota, ya golide woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Upange timaunyolo ta golide wabwino kwambiri ta pa chovala chapachifuwa, topota mwaluso ngati maukufu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Upange timaunyolo tagolide wabwino kwambiri ta pa chovala chapachifuwa, topota ngati chingwe. Onani mutuwo |