Eksodo 28:20 - Buku Lopatulika20 ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; zikhale zogwirika ndi golide m'zoikamo zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; zikhale zogwirika ndi golide m'zoikamo zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pa mzere wachinai pakhale miyala ya berili, onikisi ndi jasipere, ndipo zonsezo ziikidwe m'zoikamo zagolide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mzere wachinayi pakhale miyala ya topazi, onikisi ndi yasipa. Miyalayi uyiike mu zoyikamo zagolide. Onani mutuwo |