Eksodo 28:19 - Buku Lopatulika19 ndi mzere wachitatu wa lesemu, sibu, ndi akalama; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndi mizere wachitatu wa lesemu, sibu, ndi akalama; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Pa mzere wachitatu pakhale miyala ya yasinti, agate ndi ametisiti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 mzere wachitatu pakhale miyala ya opera, agate ndi ametisiti. Onani mutuwo |