Eksodo 28:16 - Buku Lopatulika16 Chikhale chaphwamphwa, chopindika, utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Chikhale chaphwamphwa, chopindika, utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Kukula kwake kukhale kofanana mbali zonse, ndipo chikhale chopinda paŵiri. M'litali mwake chikhale masentimita 23, muufupi mwake chimodzimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kutalika kwake kukhale kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, ndipo chikhale chopinda pawiri. Onani mutuwo |