Eksodo 28:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo uikepo miyala yoikikapo, mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo uikepo miyala yoikikapo, mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Usokererepo mizere inai ya miyala. Pa mzere woyamba pakhale miyala ya rubi, topazi ndi garaneti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Uyikepo mizere inayi ya miyala yokongola kwambiri. Mzere woyamba ukhale ndi miyala ya rubi, topazi ndi berili. Onani mutuwo |