Eksodo 27:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo uuze ana a Israele akutengere mafuta a azitona oyera opera akuunikira, kuti awalitse nyali kosalekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo uuze ana a Israele akutengere mafuta a azitona oyera opera akuunikira, kuti awalitse nyali kosalekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 “Uŵalamule Aisraele kuti akupatse mafuta aolivi opsinyidwa bwino, oyatsira nyale, kuti ziziyaka kosalekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 “Lamula Aisraeli kuti akupatse mafuta anyale a olivi wabwino kwambiri kuti nyalezo ziziyaka nthawi zonse. Onani mutuwo |