Eksodo 27:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo uzipanga nyanga zake pangodya zake zinai; nyanga zake zikhale zotuluka m'mwemo: nulikute ndi mkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo uzipanga nyanga zake pangodya zake zinai; nyanga zake zikhale zotuluka m'mwemo: nulikute ndi mkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Upange nyanga pa ngodya zake zinaizo, zilumikizane ndi guwalo, ndipo ulikute ndi mkuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Upange nyanga imodziimodzi pa ngodya zake zinayizo kuti nyangazo ndi guwalo zikhale chinthu chimodzi, ndipo ulikute guwalo ndi mkuwa. Onani mutuwo |
Tsiku lomwelo mfumu inapatulira Mulungu pakati pake pa bwalo la ku khomo la nyumba ya Yehova; pakuti pomwepo anapereka nsembe yopsereza ndi nsembe yaufa, ndi mafuta a nsembe zamtendere; popeza guwa la nsembe lamkuwa linali pamaso pa Yehova lidachepa kulandira nsembe zopsereza, ndi nsembe zaufa, ndi mafuta a nsembe zamtendere.