Eksodo 27:15 - Buku Lopatulika15 Ndi pa mbali ina pakhale nsalu zotchingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zikhale zitatu, ndi makamwa ao atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndi pa mbali ina pakhale nsalu zochingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zikhale zitatu, ndi makamwa ao atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Chimodzimodzi pa mbali ina pakhalenso nsalu zochinga, kutalika kwake mamita asanu ndi aŵiri, ndi nsanamira zitatu ndi masinde atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndipo ku mbali inayo kukhale nsalu yotchinga ya mamita asanu ndi awiri pamodzi ndi mizati itatu ndi matsinde atatu. Onani mutuwo |