Eksodo 27:14 - Buku Lopatulika14 Ndi nsalu zotchingira za pa mbali imodzi ya kuchipata zikhale za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zikhale zitatu, ndi makamwa ao atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndi nsalu zochingira za pa mbali imodzi ya kuchipata zikhale za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zikhale zitatu, ndi makamwa ao atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pa mbali ina ya chipata pakhale nsalu zochinga, kutalika kwake mamita asanu ndi aŵiri, ndi nsanamira zitatu ndi masinde atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mbali imodzi yachipata kukhale nsalu yotchinga yotalika mamita asanu ndi awiri, mizati itatu ndi matsinde atatu. Onani mutuwo |