Eksodo 27:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo m'kupingasa kwake kwa bwalo pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mukhale mikono makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo m'kupingasa kwake kwa bwalo pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mukhale mikono makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Chakuvuma, komwe kuli chipata chake, bwalolo likhalenso mamita 23 muufupi mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, kutalika kwa bwalo kukhale mamita 23. Onani mutuwo |