Eksodo 26:5 - Buku Lopatulika5 Uziika magango makumi asanu pansalu yochingira imodzi, nuikenso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; ndipo magango akomanizane lina ndi linzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Uziika magango makumi asanu pa nsalu yochingira imodzi, nuikenso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; ndipo magango akomanizane lina ndi linzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kenaka upange timagonga makumi asanu pa nsalu yoyambayo, ndipo timagonga tinanso makumi asanu pa nsalu yachiŵiriyo, kuti timagongato tiyang'anane. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Upange zokolowekamo 50 pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Upange motero kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana. Onani mutuwo |