Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Upange zokolowekamo 50 pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Upange motero kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Uziika magango makumi asanu pansalu yochingira imodzi, nuikenso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; ndipo magango akomanizane lina ndi linzake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Uziika magango makumi asanu pa nsalu yochingira imodzi, nuikenso magango makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu ya chilumikizano china; ndipo magango akomanizane lina ndi linzake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kenaka upange timagonga makumi asanu pa nsalu yoyambayo, ndipo timagonga tinanso makumi asanu pa nsalu yachiŵiriyo, kuti timagongato tiyang'anane.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:5
3 Mawu Ofanana  

Panga zokolowekamo za nsalu yobiriwira mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsiriza ya mbali ina. Uchitenso chimodzimodzi ndi nsalu yotsiriza ya mbali inayo.


Kenaka upange ngowe zagolide makumi asanu zolumikizira nsalu ziwirizo kuti zipange chihema chimodzi.


Iwo anasokerera zokolowekamo makumi asanu pa nsalu yoyamba ndi zokolowekamo makumi asanu zinanso pa nsalu inayo. Anapanga kuti zokolowekamozo ziziyangʼanana.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa