Eksodo 26:13 - Buku Lopatulika13 Ndi mkono wa pa mbali ino, ndi mkono wa pa mbali inzake, wakutsalira mu utali wake wa nsalu zophimbazo, itchinge pambali zake za chihemacho, mbali ino ndi mbali ina, kumphimba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndi mkono wa pa mbali yino, ndi mkono wa pa mbali inzake, wakutsalira m'utali wake wa nsalu za hemalo, ichinge pambali zake za Kachisi, mbali yino ndi mbali ina, kumphimba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 “Ndipo nsalu ya masentimita 46 yotsalira m'litali mwake pa mbali ziŵiri, izidzalendeŵera ndi kuphimba mbali ziŵirizo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Nsalu yotsalira ya masentimita 46 mulitali mwake mʼmbali zonse ziwiri idzalendewere kuphimba mbali ziwirizo. Onani mutuwo |