Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 26:13 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Nsalu yotsalira ya masentimita 46 mulitali mwake mʼmbali zonse ziwiri idzalendewere kuphimba mbali ziwirizo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

13 Ndi mkono wa pa mbali ino, ndi mkono wa pa mbali inzake, wakutsalira mu utali wake wa nsalu zophimbazo, itchinge pambali zake za chihemacho, mbali ino ndi mbali ina, kumphimba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndi mkono wa pa mbali yino, ndi mkono wa pa mbali inzake, wakutsalira m'utali wake wa nsalu za hemalo, ichinge pambali zake za Kachisi, mbali yino ndi mbali ina, kumphimba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 “Ndipo nsalu ya masentimita 46 yotsalira m'litali mwake pa mbali ziŵiri, izidzalendeŵera ndi kuphimba mbali ziŵirizo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:13
4 Mawu Ofanana  

Theka lotsalira la nsaluyo lidzalendewera kumbuyo kwa chihemacho.


Upange chikopa cha nkhosa zazimuna cha utoto wofiira chophimbira tentiyo ndipo pamwamba pake upangireponso chophimbira china cha zikopa za akatumbu.


Nsalu zonse zikhale zofanana. Mulitali mwake zikhale mamita khumi ndi atatu, mulifupi mamita awiri.


Nsalu zonse khumi ndi imodzi zikhale zofanana. Mulitali mwake mukhale mamita khumi ndi anayi ndipo mulifupi mwake mukhale mamita awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa