Eksodo 25:39 - Buku Lopatulika39 Achipange ichi ndi zipangizo izi zonse za talente wa golide woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Achipange ichi ndi zipangizo izi zonse za talente wa golide woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Choikaponyalecho ndi zipangizo zonse uzipange ndi golide wolemera makilogaramu 34. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Choyikapo nyale ndi zipangizo zonse zipangidwe ndi golide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34. Onani mutuwo |