Eksodo 25:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo uyang'anire uzipanga monga mwachifaniziro chao, chimene anakuonetsa m'phirimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo uyang'anire uzipanga monga mwachifaniziro chao, chimene anakuonetsa m'phirimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Usamale kuti upange zimenezi monga momwe ndikukuwonetsera paphiri pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Uwonetsetse kuti wapanga zonse monga momwe ndikukuonetsera pa phiri pano.” Onani mutuwo |