Eksodo 25:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo pa choikaponyali chomwe pakhale zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yake ndi maluwa ake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo pa choikapo nyali chomwe pakhale zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yake ndi maluwa ake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Pa choikaponyalecho padzakhale maluŵa anai a maonekedwe onga maluŵa amtowo, okhala ndi nkhunje ndi maluŵa ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pa choyikapo nyalecho pakhale zikho zinayi zopangidwa ngati maluwa amtowo ali ndi mphukira ndi maluwa. Onani mutuwo |