Eksodo 25:35 - Buku Lopatulika35 pakhale mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo, ndi mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo, ndi mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo; itere ku mphanda zisanu ndi imodzi zotuluka m'choikaponyalicho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 pakhale mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo, ndi mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo, ndi mutu pansi pa mphanda ziwiri zotuluka m'mwemo; itere ku mphanda zisanu ndi imodzi zotuluka m'choikapo nyalicho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Padzakhale nkhunje imodzi m'munsi mwake mwa magulu atatu a mphanda zija, utazipatula ziŵiriziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Mphukira yoyamba ikhale mʼmunsi mwa nthambi ziwiri zoyamba za pa choyikapo nyale. Mphukira yachiwiri ikhale mʼmunsi mwa nthambi ziwiri zinazo. Ndipo mphukira yachitatu ikhale mʼmunsi mwa nthambi zina ziwirinso. Zonse pamodzi zikhale nthambi zisanu ndi imodzi Onani mutuwo |