Eksodo 25:32 - Buku Lopatulika32 ndipo m'mbali zake mutuluke mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikaponyalicho zituluke m'mbali yake ina, ndi mphanda zitatu za choikaponyalicho zituluke m'mbali inzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 ndipo m'mbali zake mutuluke mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikapo nyalicho zituluke m'mbali yake ina, ndi mphanda zitatu za choikapo nyalicho zituluke m'mbali inzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pa mbali zake pakhale mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu pa mbali iliyonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Mʼmbali mwake mukhale mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu mbali iliyonse. Onani mutuwo |