Eksodo 25:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo uziika mkate woonekera pa gomelo pamaso panga nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo uziika mkate woonekera pa gomelo pamaso panga nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Patebulopo uziikapo buledi woperekedwa kosalekeza, kuti azikhala pamaso panga nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Pa tebulopo uyikepo buledi woperekedwa kosalekeza, kuti azikhala pamaso panga nthawi zonse. Onani mutuwo |
Taonani, nditi ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba, kumpatulira iyo, ndi kufukiza pamaso pake zonunkhira za fungo lokoma, ndiyo ya mkate woonekera wachikhalire, ndi ya nsembe zopsereza, m'mawa ndi madzulo, pamasabata, ndi pokhala mwezi, ndi pa zikondwerero zoikika za Yehova Mulungu wathu. Ndiwo machitidwe osatha mu Israele.