Eksodo 25:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo choperekacho uchilandire kwa iwo ndi ichi: golide, ndi siliva, ndi mkuwa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo choperekacho uchilandire kwa iwo ndi ichi: golide, ndi siliva, ndi mkuwa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zopereka zimene ulandirezo ndi izi: golide, siliva, mkuŵa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Zopereka zimene ulandire kwa anthuwo ndi izi: Golide, siliva ndi mkuwa. Onani mutuwo |