Eksodo 25:2 - Buku Lopatulika2 Lankhula ndi ana a Israele, kuti anditengere chopereka; ulandire chopereka changa kwa munthu aliyense mtima wake umfunitsa mwini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Lankhula ndi ana a Israele, kuti anditengere chopereka; ulandire chopereka changa kwa munthu aliyense mtima wake umfunitsa mwini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Uza Aisraele apereke zopereka zao kwa Ine. Tsono iwe ulandire zoperekazo kwa munthu aliyense wa mtima wofuna kupereka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Uza Aisraeli kuti abweretse chopereka kwa Ine. Iwe ulandire choperekacho mʼmalo mwanga kuchokera kwa munthu amene akupereka mwakufuna kwake. Onani mutuwo |