Eksodo 25:19 - Buku Lopatulika19 Nupange kerubi mmodzi ku thungo lino, ndi kerubi wina ku thungo lina; upange akerubi ochokera kuchotetezerapo, pa mathungo ake awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Nupange kerubi mmodzi ku thungo lino, ndi kerubi wina ku thungo lina; upange akerubi ochokera kuchotetezerapo, pa mathungo ake awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 wina uku wina uku. Akerubiwo uŵalumikize ndi chivundikiro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 kerubi mmodzi mbali ina ndi wina mbali inayo. Akerubiwa uwapangire limodzi ndi chivundikirocho mʼmapeto mwa mbali ziwirizo. Onani mutuwo |