Eksodo 25:18 - Buku Lopatulika18 Uzipanganso akerubi awiri agolide; uwasule mapangidwe ake, pa mathungo ake awiri a chotetezerapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Uzipanganso akerubi awiri agolide; uwasule mapangidwe ake, pa mathungo ake awiri a chotetezerapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pa mbali ziŵiri za chivundikirocho, m'mphepete mwake, upange akerubi aŵiri, agolide, osula ndi nyundo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo upange Akerubi awiri agolide osula ndi nyundo, uwayike mbali ziwiri za chivundikirocho, Onani mutuwo |