Eksodo 25:14 - Buku Lopatulika14 Nupise mphiko m'mphetezo pa mbali zake za likasa, zakunyamulira nazo likasalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Nupise mphiko m'mphetezo pa mbali zake za likasa, zakunyamulira nazo likasalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Mphiko zimenezo udzazilonge m'mphetezo pa mbali ziŵiri za bokosilo, kuti azinyamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo ulowetse nsichizo mʼmphete zija za mbali zonse ziwiri za bokosilo kuti azinyamulira. Onani mutuwo |