Eksodo 25:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo uzipanga mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi golide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo uzipanga mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi golide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Upangenso mphiko zakasiya, ndipo mphikozo uzikute ndi golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kenaka upange mizati yamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide. Onani mutuwo |