Eksodo 25:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo uliyengere mphete zinai zagolide, ndi kuziika kumiyendo yake inai; mphete ziwiri pa mbali yake ina, ndi mphete ziwiri pa ina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo uliyengere mphete zinai zagolide, ndi kuziika kumiyendo yake inai; mphete ziwiri pa mbali yake ina, ndi mphete ziwiri pa ina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Upange mphete zinai zagolide zonyamulira bokosilo, ndi kumangirira mphetezo ku miyendo yake inai, uku ziŵiri uku ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Upange mphete zinayi zagolide ndipo uzimangirire ku miyendo yake inayi ya bokosilo, mbali ina ziwiri ndi mbali inanso ziwiri. Onani mutuwo |