Eksodo 25:15 - Buku Lopatulika15 Mphiko zikhale m'zimphete za likasa; asazisolole. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Mphiko zikhale m'zimphete za likasa; asazisolole. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mphikozo zidzangokhala m'mphetezo osazitulutsanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Nsichizo zizikhala mʼmphete za bokosilo nthawi zonse, zisamachotsedwe. Onani mutuwo |