Eksodo 23:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo samalirani zonse ndanena ndi inu; nimusatchule dzina la milungu ina; lisamveke pakamwa pako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo samalirani zonse ndanena ndi inu; nimusatchule dzina la milungu ina; lisamveke pakamwa pako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mumvetse zonse zimene ndakuuzanizi. Musamapemphera kwa milungu ina, ndi maina ake omwe musamaŵatchula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “Samalani pochita zonse zimene ine ndanena. Musamapemphere kwa milungu ina ndipo mayina awo musamawatchule. Onani mutuwo |