Eksodo 22:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo muzindikhalira Ine anthu opatulika; chifukwa chake musamadya nyama yojiwa kuthengo; itayireni agalu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo muzindikhalira Ine anthu opatulika; chifukwa chake musamadya nyama yojiwa kuthengo; itayireni agalu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Mudzakhale anthu operekedwa kwa Ine. Motero musadzadye nyama ya choŵeta chilichonse chojiwa ndi zilombo ku thengo. Nyama imeneyo mudzapatse agalu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Inu mukhale anthu anga opatulika. Choncho musadye nyama ya chiweto chimene chaphedwa ndi zirombo. Nyamayo muwaponyere agalu.” Onani mutuwo |