Eksodo 22:16 - Buku Lopatulika16 Munthu akanyenga namwali wosapalidwa ubwenzi, nakagona naye, alipetu kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Munthu akanyenga namwali wosapalidwa ubwenzi, nakagona naye, alipetu kuti akhale mkazi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Munthu akanyenga namwali wosadziŵa mwamuna, yemwe sanatomeredwe, nagona naye, alipire chiwongo, ndipo amkwatire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Ngati munthu anyenga namwali wosadziwa mwamuna amene sanapalidwe ubwenzi ndi kugona naye, munthuyo ayenera kulipira malowolo ndipo adzakhala mkazi wake. Onani mutuwo |