Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 21:5 - Buku Lopatulika

5 Koma mnyamatayo akanenetsa, Ndikonda mbuye wanga, mkazi wanga, ndi ana anga; sindituluka waufulu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma mnyamatayo akanenetsa, Ndikonda mbuye wanga, mkazi wanga, ndi ana anga; sindituluka waufulu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Koma kapoloyo akanena kuti, ‘Ndimakonda mbuyanga, mkazi wanga ndi ana anga, sindifuna kuti ndimasulidwe,’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 “Koma ngati kapoloyo alengeza kuti, ‘Ine sindikufuna kumasulidwa chifukwa ndimakonda mbuye wanga, mkazi wanga ndi ana,’

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:5
5 Mawu Ofanana  

Akampatsa mkazi mbuye wake, ndipo akambalira ana aamuna ndi aakazi, mkaziyo ndi ana ake azikhala a mbuye wake, ndipo azituluka ali yekha.


pamenepo mbuye wake azifika naye kwa oweruza, nafike naye kukhomo, kapena kumphuthu, ndipo mbuye wake am'boole khutu lake ndi lisungulo; ndipo iye azimgwirira ntchito masiku onse.


Yehova Mulungu wathu, pamodzi ndi Inu Ambuye ena adatilamulira ife; koma mwa Inu nokha tidzatchula dzina lanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa